Sat Apr 20 2024 09:35:07 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-20 09:35:08 +02:00
parent ba77fda69b
commit c95a2cda0d
3 changed files with 3 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 \v 10 Choncho Yezebeli analemba makalata mdzina la Ahabu, nawadinda ndi chidindo chake, nkuwatumiza kwa akulu ndi kwa olemekezeka amene anakhala naye mmisonkhano, amene anali kukhala pafupi ndi Naboti. \v 9 Iye analemba mmakalatawo kuti: “Lalikirani kusala kudya ndipo mukhazikitse Naboti pamwamba pa anthuwo. amponye miyala kuti afe.
\v 8 \v 10 Choncho Yezebeli analemba makalata mdzina la Ahabu, nawadinda ndi chidindo chake, nkuwatumiza kwa akulu ndi kwa olemekezeka amene anakhala naye mmisonkhano, amene anali kukhala pafupi ndi Naboti. \v 9 Iye analemba mmakalatawo kuti: “Lalikirani kusala kudya ndipo mukhazikitse Naboti pamwamba pa anthuwo. Mutengerenso amuna awiri opanda pake kuti amchitire umboni kuti, Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu.’” Kenako mumtulutseni ndi kumuponya miyala kuti afe.

1
21/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 \v 14 Choncho amuna a mumzinda wa Naboti, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzinda wa Naboti, anachita monga mmene Yezebeli anawafotokozera, monga mmene zinalembedwera mmakalata amene anawatumizira. \v 12 Iwo analengeza kuti kusala kudya nkukhazika Naboti pamwamba pa anthu. \v 13 Anthu awiri achinyengowo analowa ndi kukhala pamaso pa Naboti; ndipo anamchitira umboni Naboti pamaso pa anthu, kuti, Naboti watemberera Mulungu ndi mfumu. Kenako anamutengera kunja kwa mzinda ndi kumuponya miyala. Kenako akuluwo anatumiza uthenga kwa Yezebeli kuti: “Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa.

View File

@ -388,7 +388,7 @@
"21-01",
"21-03",
"21-05",
"21-11",
"21-08",
"21-15",
"21-17",
"21-19",