diff --git a/21/08.txt b/21/08.txt index 774cdac..546f26e 100644 --- a/21/08.txt +++ b/21/08.txt @@ -1 +1 @@ -\v 8 \v 10 Choncho Yezebeli analemba makalata m’dzina la Ahabu, nawadinda ndi chidindo chake, n’kuwatumiza kwa akulu ndi kwa olemekezeka amene anakhala naye m’misonkhano, amene anali kukhala pafupi ndi Naboti. \v 9 Iye analemba m’makalatawo kuti: “Lalikirani kusala kudya ndipo mukhazikitse Naboti pamwamba pa anthuwo. amponye miyala kuti afe. \ No newline at end of file +\v 8 \v 10 Choncho Yezebeli analemba makalata m’dzina la Ahabu, nawadinda ndi chidindo chake, n’kuwatumiza kwa akulu ndi kwa olemekezeka amene anakhala naye m’misonkhano, amene anali kukhala pafupi ndi Naboti. \v 9 Iye analemba m’makalatawo kuti: “Lalikirani kusala kudya ndipo mukhazikitse Naboti pamwamba pa anthuwo. Mutengerenso amuna awiri opanda pake kuti am’chitire umboni kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu.’” Kenako mum’tulutseni ndi kumuponya miyala kuti afe. \ No newline at end of file diff --git a/21/11.txt b/21/11.txt new file mode 100644 index 0000000..c171668 --- /dev/null +++ b/21/11.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 11 \v 14 Choncho amuna a mumzinda wa Naboti, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzinda wa Naboti, anachita monga mmene Yezebeli anawafotokozera, monga mmene zinalembedwera m’makalata amene anawatumizira. \v 12 Iwo analengeza kuti kusala kudya n’kukhazika Naboti pamwamba pa anthu. \v 13 Anthu awiri achinyengowo analowa ndi kukhala pamaso pa Naboti; ndipo anamchitira umboni Naboti pamaso pa anthu, kuti, Naboti watemberera Mulungu ndi mfumu. Kenako anamutengera kunja kwa mzinda ndi kumuponya miyala. Kenako akuluwo anatumiza uthenga kwa Yezebeli kuti: “Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index ced0512..cf01f29 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -388,7 +388,7 @@ "21-01", "21-03", "21-05", - "21-11", + "21-08", "21-15", "21-17", "21-19",