Sat Apr 20 2024 09:55:09 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-20 09:55:12 +02:00
parent 7648858dc1
commit 39e78b51de
4 changed files with 4 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 33 Ndipo mfumu ya Aramu inalamulira akapitao makumi atatu mphambu awiri a magareta ace, ndi kuti, Musakantha ankhondo ang'ono kapena omveka; \v 32 Ndipo panali pamene akapitao a magareta anaona Yehosafati, anati, Zoonadi, ameneyo ndiye mfumu ya Israyeli. Iwo anatembenuka kuti amenyane naye, choncho Yehosafati analira. Ndiyeno akuluakulu a magaletawo ataona kuti si mfumu ya Isiraeli, anabwerera osamuthamangitsa.
\v 31 Ndipo mfumu ya Aramu inalamulira akapitao makumi atatu mphambu awiri a magareta ace, ndi kuti, Musakantha ankhondo ang'ono kapena omveka; \v 32 Ndipo panali pamene akapitao a magareta anaona Yehosafati, anati, Zoonadi, ameneyo ndiye mfumu ya Israyeli. Iwo anatembenuka kuti amenyane naye, choncho Yehosafati analira. \v 33 Ndiyeno akuluakulu a magaletawo ataona kuti si mfumu ya Isiraeli, anabwerera osamuthamangitsa.

1
22/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Koma munthu wina anaponya uta wake mwachisawawa, nalasa mfumu ya Israyeli pakati pa mfundo za zida zake. Pamenepo Ahabu anauza woyendetsa galeta lake kuti: “Tembenuka unditulutse kunkhondo, pakuti ndavulala kwambiri.

1
22/35.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Nkhondoyo inakula tsiku lomwelo, ndipo mfumu inaimitsidwa mgaleta lake pamaso pa Aaramu. Iye anafa madzulo. Mwazi unatuluka mbalalo nkulowa pansi pa gareta. Pamenepo dzuwa linali kulowa, anthu anafuula kuti: “Aliyense abwerere kumudzi wake, ndipo aliyense abwerere kudera lake.

View File

@ -410,8 +410,8 @@
"22-24",
"22-26",
"22-29",
"22-31",
"22-34",
"22-35",
"22-37",
"22-39",
"22-41",