Sat Apr 20 2024 09:53:09 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-20 09:53:10 +02:00
parent b6870ffbfc
commit 7648858dc1
4 changed files with 4 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 26 \v 27 Mfumu ya Isiraeli inauza mtumiki wake kuti: “Mgwire Mikaya ndi kupita naye kwa Amoni kazembe wa mzindawo, ndi kwa Yowasi mwana wanga. mkate wa nsautso ndi madzi a nsautso mpaka ndikafike bwinobwino.’” \v 28 Pamenepo Mikaya anati: “Mukabwerera bwinobwino, ndiye kuti Yehova sananene mwa ine. Kenako anawonjezera kuti: “Mverani izi, anthu nonsenu.
\v 26 Mfumu ya Isiraeli inauza mtumiki wake kuti: “Mgwire Mikaya ndi kupita naye kwa Amoni kazembe wa mzindawo, ndi kwa Yowasi mwana wanga. \v 27 Amunene kuti, Mfumu ikuti, Ikani munthu uyu mndende, ndipo mumpatse chakudya cha nsautso ndi madzi a nsautso kufikira ndikadzabwera mwamtendere. \v 28 Pamenepo Mikaya anati: “Mukabwerera bwinobwino, ndiye kuti Yehova sananene mwa ine. Kenako anawonjezera kuti: “Mverani izi, anthu nonsenu.

1
22/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Choncho Ahabu mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anapita ku Ramoti Giliyadi. \v 30 Mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha ndi kupita kunkhondo, koma iwe vala zovala zako zachifumu. Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha + nkupita kunkhondo.

1
22/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 \v 33 Ndipo mfumu ya Aramu inalamulira akapitao makumi atatu mphambu awiri a magareta ace, ndi kuti, Musakantha ankhondo ang'ono kapena omveka; \v 32 Ndipo panali pamene akapitao a magareta anaona Yehosafati, anati, Zoonadi, ameneyo ndiye mfumu ya Israyeli. Iwo anatembenuka kuti amenyane naye, choncho Yehosafati analira. Ndiyeno akuluakulu a magaletawo ataona kuti si mfumu ya Isiraeli, anabwerera osamuthamangitsa.

View File

@ -408,8 +408,8 @@
"22-18",
"22-21",
"22-24",
"22-26",
"22-29",
"22-31",
"22-34",
"22-35",
"22-37",