nyu_mrk_text_reg/15/16.txt

1 line
292 B
Plaintext

\v 16 \v 17 \v 18 Tsono asilikali adamutengera ku mbuto ya chiyeruzo(komwe kuli ku likulu la boma), adachemerezana wense pabodzi asilikali wa boma. Adabzazika chaku bzala chifwira Yesu, achisona chipewu chaminga achibzazika iye. Achiyamba kusenzeka naye achiti, ''Tikuoneni, mpfumu ya Yuda!''