nyu_mrk_text_reg/07/29.txt

1 line
215 B
Plaintext

\v 29 Iye adalewa kuna iye, ''Thangwe la bzomwe walewa, podi kuyenda. Chiwanda mwa mwanako chachoka.'' \v 30 Iye adabwerera kuyenda kumuyi kwache achikagumana mwanayo atagona pa talima, na chiwandacho chita choka.