nyu_mrk_text_reg/01/35.txt

1 line
211 B
Plaintext

\v 35 Iye adabesera kumuka, kukana mdima, adawaleka achiyenda kumbuto ya chete kukapemba. \v 36 Simoni na anzache adamuyang'ana yang'ana iye. \v 37 Adakamugumana achimuuza iye, ''Wanthu wense akukuyang'anani.''