nyu_mrk_text_reg/01/23.txt

1 line
384 B
Plaintext

\v 23 Tsono pomwepo pakhana munthu ntchalitchimo wa nzimu wakuyipa adakuwa, \v 24 achiti, ''Tilinamwe chani ife, Yesu wa kunazaleti? Wabwera kudzati dzonga ife? Ine ndikukudziwani. Ndimwe m'bodzi wakuchena wa Mulungu!'' \v 25 Yesu adatsimula chiwanda achiti, ''Nyamala ndipo uchoke mwa uyu!'' \v 26 Tsono nzimu wakuyipa udachoka mwa iye uchiyenda kutali pomwe adakuwa namafala makulu.