nyu-ml-nyungwe_mrk_text_reg/15/36.txt

1 line
297 B
Plaintext

\v 36 Winango adathamanga, ikani chibvenje adachiyika icho ku psimbo, adampasa iye kuti amwe. Payi achiti, ''Dikirani tiwone ngati Yeliyayo abwera kudzam'bulusa pansi.'' \v 37 Ndipo Yesu adalira namafala makulu mkufa. \v 38 Chiguwo chatchalitchi chidang'ambika kuchokera pa dzawulu kukafika pansi.