nyu-ml-nyungwe_mrk_text_reg/08/22.txt

1 line
313 B
Plaintext

\v 22 Iwo adayenda ku Betisaida.Wanthu adabwera naye munthu zimola kuna iye achikumbira Yesu kuti am'phate iye. \v 23 Yesu adam'phata boko munthu zimolayo achi choka naye kunja kwa muyi. Pamene adapsipirara mata m'maso mwaso mwache achi sanjika manja pa iye , iyeadabvunza iye, ''Ukuona chinthu chili chense?''