Tue Oct 10 2023 11:56:22 GMT+0200 (Hora da África Central)

This commit is contained in:
tsDesktop 2023-10-10 11:56:23 +02:00
parent 393a550721
commit 0a261257f0
3 changed files with 5 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 33 \v 34 \v 35 Panthawi ya chitanthatu, mndima udagwa pa dziko lense lapansi kufikira lachipfemba. Panthawi yachi pfemba Yesu adalira namafala makulu, ''Eloi,Eloi, lamasabakata?'' Bzomwe bzikhalewa kuti, ''Mulungu wangu, mulungu wangu, thangwe lanyi mwandisiya ndekha?'' Iwo omwe akhali pafipi adabza kukuwa kwache achiti, ''Onani, iye akuchemera Yeliya.''
\v 33 Panthawi ya chitanthatu, mndima udagwa pa dziko lense lapansi kufikira lachipfemba. \v 34 Panthawi yachi pfemba Yesu adalira namafala makulu, ''Eloi,Eloi, lamasabakata?'' Bzomwe bzikhalewa kuti, ''Mulungu wangu, mulungu wangu, thangwe lanyi mwandisiya ndekha?'' \v 35 Iwo omwe akhali pafipi adabza kukuwa kwache achiti, ''Onani, iye akuchemera Yeliya.''

View File

@ -1 +1 @@
\v 36 \v 37 \v 38 Winango adathamanga, ikani chibvenje adachiyika icho ku psimbo, adampasa iye kuti amwe. Payi achiti, ''Dikirani tiwone ngati Yeliyayo abwera kudzam'bulusa pansi.'' Ndipo Yesu adalira namafala makulu mkufa. Chiguwo chatchalitchi chidang'ambika kuchokera pa dzawulu kukafika pansi.
\v 36 Winango adathamanga, ikani chibvenje adachiyika icho ku psimbo, adampasa iye kuti amwe. Payi achiti, ''Dikirani tiwone ngati Yeliyayo abwera kudzam'bulusa pansi.'' \v 37 Ndipo Yesu adalira namafala makulu mkufa. \v 38 Chiguwo chatchalitchi chidang'ambika kuchokera pa dzawulu kukafika pansi.

View File

@ -178,6 +178,8 @@
"15-22",
"15-25",
"15-29",
"15-31"
"15-31",
"15-33",
"15-36"
]
}