\v 15 Wense alinaine kuno, akukumonisa.Amonise wense iwepo amatikonda mwachikhulupiriro. Ntendele ukhale kwamwese.