kdn_rom_text_reg/01/08.txt

1 line
325 B
Plaintext

\v 8 Chakuyamba nitenda Mulungu wangu kuchokela mwaYesu kristu naimwe mwentse, pakuti chikhulupililo chanu chinichemelewa kuchokela pantsi lentse. \v 9 Mulungu ndichapupu changu pomwe ndine mutumiki wafala lamwana wake. \v 10 Ndimbakhala ndichimbakukumbililani kuti ndikhale wakupiyilila nakufuna kwaMulungu pakubwela kwanu.