sbs-x-chiikuhane_luk_text_reg/01/26.txt

1 line
408 B
Plaintext

\v 26 \v 27 \v 28 \v 29 Mumwezi wa chisanu nakamozi, mungelo Gabriel antumiwa ndi Mulungu kumuzinda oitaniwa nazaleti, kulinamwali wamene anali okobekelewa ku mwamuna wa zina la Yosefe. Analikuchokela munyumba ys Davidi, ndi zina yanamwali inali Mariya.Anabwela kwa iye ndikunene, '' Mulibwanji, inu odala! Ambuye alinanu.'' Koma anankala osokonezeka pamau yake ndikudabwa kuti kodi ungankhale moni wabwanji.