sbs-x-chiikuhane_luk_text_reg/01/21.txt

1 line
372 B
Plaintext

\v 21 \v 22 \v 23 Koma manje banthu banali kuembekeza Zakaliya, chenze kubadabwisa chifukwa chakuti enze kutayanthawi yambili mu tempele. koma pamene anachoka, sianali kukamba nabemve.Anazindikila kuti anaona mansompenya pamene anali mutempele. Anapitiliza kualangiza ziziwiso ndi kunkhala kachete.pamene nthawi ya masiku yake yotumikila yanasila, anayenda kunyumba kwake.