sbs-x-chiikuhane_luk_text_reg/01/18.txt

1 line
488 B
Plaintext

\v 18 \v 19 \v 20 Zakaliya ananena kwa mungelo, ''Kodi ninkazibe bwanji izi? chifukwa ndine okalamba ndi mukazi wanga naemve ni mukukulu.'' Mungelo anayankha ndikunena kwa iye, '' Ndine Gabuliyele,wamene amaimila pamanso ya Mulungu.Nenze natumiwa kulankula naiwe,kubwelesa uyu utenga wabwino.Ndiponso, uzankhala mwakacheta, ndikukangiwa kukamba, kufikila siku yamene izi zinthu zizafikiliziwa.Ichi nichifukwa chakuti, siuna kululupile mau yanga, yamene yazafikilisiwa pa nthawi yokwana.''