sbs-x-chiikuhane_luk_text_reg/01/16.txt

1 line
299 B
Plaintext

\v 16 \v 17 Ndiponso banthu bambili baku isilaeli, bazapindimukila kwa Mulungu wao.Azaenda pamanso ya Mulungu mu muzimu ndi mphamvu za Eliya.Azachita izi pakupindimula mitima yabazitate kubanababo, kuti, ajaosamvelela baende munzelu zaolungama- ndikupanga banthu kukonzeka, ndikukonzekela Mulungu''.