sbs-x-chiikuhane_luk_text_reg/01/11.txt

1 line
333 B
Plaintext

\v 11 \v 12 \v 13 Manje mungelo wa Mulungu anaonekela kwa iye ndikuimilila kumbali ya zanja lamanja yaguwa yansembe.Pamene Zachaliya anamuna, Iye anaopezedwa ndi Mantha. Koma mungelo ananena kwaiye, ''Usayope Zachaliya, chifukwa mapempelo yako zamveka.mukazi wako Elizabeta azakubalila mwana mwamuna.uzamuitana zinalache kuti Yohane.