nya-x-nyanja_luk_text_reg/05/18.txt

1 line
397 B
Plaintext

\v 18 \v 19 Koma bamuna bena bana bwela, ananyamula pampasa mwamuna wamene sianali kuyenda, Ndiponso anaona njila yomubweleselamo mukati pakuti amufake kuntangu na Yesu kuti amufakepo zanja.Sibana pezenjila yomupelekelamo mukati chifukwa kunali chigulu chabanthu, kamba kaichi banaenda pamwamba pa nyumba ndiponso banamuselusila pansi, pa mpasa yake, pakatika banthu, pantangu pamene analili Yesu.