nya-x-nyanja_luk_text_reg/05/12.txt

1 line
304 B
Plaintext

\v 12 \v 13 Chinabwela chachitika kuti pamene akali mumuzinda winangu, Munthu wamene anali ndi lepulosi analipo, Pamene anaona Yesu anagwesa manso yake ndi kumupempa, nakunena, ''Abuye, ngati mufuna, nitubiseni.'' Ndipo Yesu antambusula kwanja kwake ndi kumugwila, nakunena, ''Nifuna, nkhala otubisiwa.''