1 line
278 B
Plaintext
1 line
278 B
Plaintext
\v 34 \v 35 Mariya ananena ku mungelo, ''Kodi izi zichitika bwanji, popeza kuti sininagonepo na mwamuna?'' Mungelo anayankha ndikunena kwa iye, ''Muzimu oyela azabwela pali iwe, ndi mphamvu zawakumwamba zizabwela pali iwe. koma oyela wamene azabadwa azaitaniwa mwana wa Mulungu. |