nya-x-nyanja_luk_text_reg/05/14.txt

1 line
222 B
Plaintext

\v 14 Anamuuza kuti asauze aliyense, Koma anamuuza, '' Kuti enda njila yako, Ndiponso ukazilangize kuopeleka ansembe ndiponso upeleke chansembe pakutubisiwa kwako, kulinganiza mwane mose analamulila, monga umboni kwaiwo.''