nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/46.txt

1 line
452 B
Plaintext

\v 46 \v 47 \v 48 Nichifukwa chani chamene muniitanila, 'Ambuye, Ambuye,' ndiponso simumvelela zinthu zamene nikuuzani? Alionse wamene abwela kwaine ndiponso nakumvelela mau yanga, Nizakuuzani mwamene alili.Ali monga munthu wamene amanga nyumba, wamene anakumba pansi pantaka ndiponso nakumanga chi manyumba pamwala olimba.pamene kuziliwa kwamanzi kunabwela, kupopota kwamanzi kunachaya nyumba ija, koma siinagwedezeke, chifukwa yenze inamangiwa bwino.