nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/45.txt

1 line
224 B
Plaintext

\v 45 Munthu wabwino kuchokela muchipao chaubwinowake wamumutima amabeleka za bwino, ndiponso munthu oyipa kuchokela muchipao chakuipa kwamumutima wake amabeleka zoipa. Koma kuchokela mu unyinji waza mumutima kamwa kazanena.