nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/31.txt

1 line
430 B
Plaintext

\v 31 \v 32 \v 33 \v 34 Monga mwanene ufuna banthu bena kukuchitila, Naiwe uchite chimodzimodzi kulibemve. Ngati ukonda chabe baja bamene bakukonda, Kodi nipindu bwanji yamene ingankale kwaiwe? chifukwa ndi ochimwa akonda kuchita chimodzimodzi. Ngati ukongolesa chabe kuli banthu bamene uganizila kuti ndibemve bazakubwezelanso, Kodi nipindu bwanji iyo kuliiwe? Ndi ochimwa amakongolesa kuochimwa, kuti alandile mumuyeselo umodzi.