\v 29 \v 30 Kuli iwo bamene bakumenyani kutobo, mupasenso ndi kwinakwache.Ngati munthu wina atenga koti yako, usagwilililenso chovala chako. Pasa aliyense wamene akupempa.Ngati munthu wina atenga chinthu chako, usamufunse kuti akubwezele.