nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/22.txt

1 line
296 B
Plaintext

\v 22 \v 23 Ndimwe odala ngati banthu banthu bakuzondani ndiponso kukupatulani ndiponso kukutukwanani, chifukwa chamwana wa munthu. Sekelelani muli ija siku ndiponso ndi chimwemwe, chifukwa muzankhala ndi mphatso yaikulu kuchoka kumwamba, ndi mibado yao inachita kuaneneli babo munjila imozimozi.