nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/17.txt

1 line
479 B
Plaintext

\v 17 \v 18 \v 19 Koma Yesu anabwela pansi paluphiri ndi iwo nakuimilila pamalo pamene panali polingana ndi ophunzila bake bambiri ndiponso gulu ikulu yabathu baku Judeya ndiponso Jelusalemu ndiponso akuchimana chaku Tyre ndiponso Sidoni. Banabwela kumvelela kwaiye ndiponso kuchilisiwa kumatenda yao. Banthu bamene anavutisiwa ndi mizimu zonyansa anachilisiwa.Alionse mugulu analikuyeselela kumugwila chifukwa mphanvu zochilisa zinalikuchoka mwaiye, ndiponso anabachilisa bonse.