nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/06.txt

1 line
502 B
Plaintext

\v 6 \v 7 \v 8 Chinachitika pa sabata inangu pamene anaenda musinagogi ndi kuuza banthu bena muja.Munali mwamuna muja wamene anali nazanjalamanja lolemala.Akalembela ndi afalisi analikumuyangana chabe pafupipafupi nakuona ngati azapolesa wina pasabata, pakuti bapezelepo chifukwa chomuzuzulilapo. Koma anaziba zamene banali kuganiza ndiponso ananena kuli mwamuna wamene kwanja yake inali yolemala, ''Anati ima, ndiponso uimilile pakati palialionse.'' Ndiponso mwamuna anaima ndiku imilila pamene paja.