nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/03.txt

1 line
460 B
Plaintext

\v 3 \v 4 \v 5 Ndiponso pakumuyankha iye, Yesu ananena, ''Kodi siunabelenge vamene David anachita pamene enze nanjala, Iye ndiponso nabamene analinabo? Anaenda munyumba ya Mulungu, nakutenga mukate wamene unali munso yake ndi kudyapo mbali yamukate, ndiponso anatengapo mukate wina nakupasa amuna bamene analinao kuti badye, angankhale chinali chabe chovomelezewa kuopeleka ansembe kudya.'' Ndiponso ananena kwaiyo, ''Kuti mwana wamuthu ni Mulungu wa sabata.''