nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/01.txt

1 line
348 B
Plaintext

\c 6 \v 1 \v 2 Manje chinabwela chachitika pa sabata kuti Yesu analikuyenda mumunda mwamene balima mbeu ndiponso bopunzila bake banali kudoba mitu zambeu, ndikuzinyanyaula mumanja yao ndiponso banalikudwa izi mbeu, Koma wina wa afalisi ananena, '' Kodi nichifukwa chachani chamene muchitila chinthu chamene sicholamulidwa kuchita pasikula sabata?''