nya-x-nyanja_luk_text_reg/03/18.txt

1 line
298 B
Plaintext

\v 18 \v 19 \v 20 Ndi bambiri enanso ozinyamula, Yoani analalikila utenga wabwino kubanthu. Pamene Herodi ndi tetrachi bana vomekezedwa kukwatila mukazi wamubale wao, Helodias, ndi zinthu zonse zonyansa zamene anachita ndi Helod, anafakilako pamilandu zonse zamene anachita: anakomela Yoani mujele.