nya-x-nyanja_luk_text_reg/03/15.txt

1 line
391 B
Plaintext

\v 15 \v 16 Koma pamene banthu banali ndi chilakolako kuembekeza kubwela kwa kristhu, aliyense anali kuzifufuza mumitima mwao paza Yoani ngati angankale kristhu. Yoani anabayankha bonse, '' koma ine, nikubadizani ndi manzi, koma alikubwela winawake wamene alina mphamvu kupambana ine, ndiponso siniyenela ndi kumasula ntambo zansapato zake.Azakubadizani ndi muzimu oyela ndiponso ndi mulilo.