nya-x-nyanja_luk_text_reg/03/10.txt

1 line
273 B
Plaintext

\v 10 \v 11 Ndipo aya magulu yanapitiliza kumufunsa, ndikunene, ''Kuti kansi tingachite bwanji?'' Iye anabayanka, ndi kunena kuli iwo, ngati winawache alina na zovala zibili, afunika kugabana ndi mumunthu wamene alibe, ndi uja alina zakudya afunikila kuchita chimozimozi.''