nya-x-nyanja_luk_text_reg/03/07.txt

1 line
170 B
Plaintext

\v 7 Ndipo Yoani ananena ku magulu yakulu yabanthu bamene banali kubwela kubadizika ndi iye, '' imwe bana banjoka!nindani ukuchenjezani kuti mutabe kuukali wamene ubwela?