nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/41.txt

1 line
531 B
Plaintext

\v 41 \v 42 \v 43 \v 44 Makolo bake banalikuyenda chaka chilichonse ku Yelusalemu kumadyelelo ya paskha.Pamene anali ndi zaka makumi yabili ndi tubili, banaendanso panthawi ya mwambo wa madyelelo.Kuchekela pamene banankhalako masiku yokwana yamadyelelo, anayamba kubwelelamo ku nyumba kwao.Koma munyamata Yesu anasalila mu Yelusalema ndiponso makolo yake sibanazibe.Banalikuganizila kuti kapena alinagulu yamene anali nao pamodzi, koma anaenda ulendo uyu siku limozi.Ndiponso anayamba kumusakila kuliba banja lao ndi pa abwenzi ao.