nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/36.txt

1 line
499 B
Plaintext

\v 36 \v 37 \v 38 Muneneli otanidwa zina Anna analiko. analimwana mukazi wa faniwelo kuchoka mumutundu wa Asha.Anali mukulu maningi.Anankhala na mwamuna wake zaka makumi ndi awiri kuchokela kuunamwali wake, ndiponso anali ofelewa zaka 80.Sianachokepo mutempele chifukwa analikutumikila mumapempelo ndi kusala kudya, usiku ndi muzuba. pali ijanthawi, anabwela kulibemve ndiponso anayamba kupeleka matamando kwa Mulungu ndi kukamba pa mwana kwa alionse analiku kuembekezela chipulumuso cha Yelusalemu.