nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/17.txt

1 line
428 B
Plaintext

\v 17 \v 18 \v 19 \v 20 Pochekala kumuona,analengesa kuziba chamene chinauziwa kuli bemve pamwana uyu.Bonse bamene bana mvela banali odabwisiwa ndichamene anauziwa nabaja oyembela.Koma Mariya anangopitiliza kuganizila pazinthu zonse zamene anamvela, ndi kuzisungilila mumutima wake. Oyembela anabwelamo, ndiponso analikulemekeza ndi kutamanda Mulungu palizonse zamene banamvela ndi kuona, monga mwamene chinakambidwa kuli benve.