nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/15.txt

1 line
319 B
Plaintext

\v 15 \v 16 Chinabwela chachitika kuti pamene angelo anachoka pamalo yao ndi kuyenda kumwamba, oyembela ngo'mbe anazi uza iwo oka, '' Tiyeni manje ku batilehemu, tikaone ichi chamene chachitika, chamene amuye alengesa kuti ise tizibe.'' Anaendisa kuyenda ndiponso anapeza Mariya ndi Yosefe, nakupeza mwana agona mukola.