nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/08.txt

1 line
217 B
Plaintext

\v 8 \v 9 Kunali boyembela ngo'mbe muja muchigao bamene banalikunkhala muminda, kuyembela ngo'mbe zao usiku.Mungelo wa Mulungu anaonekela kwa iwo, ndi ulrmelelo wa Mulungu unalangisiwa kuli bemve, ndiponso anayofedwa.