nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/06.txt

1 line
260 B
Plaintext

\v 6 \v 7 Manje chinabwela chachitika kuti pamene bakalikwamenekuja, nthawi inafika yobala. Anabala mwana mwamuna, mwana wake oyamba, ndiponso anamu vininkila na nyula yopitamo milaini, ndiponso nakumufaka mukola, chifukwa kunalibe malo muja mwamene anafikila.