nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/01.txt

1 line
288 B
Plaintext

\c 2 \v 1 \v 2 \v 3 Koma muli yaja masiku,chinabwela chachitika kuti Siza Ogastasi anatuma mbiri yakuti kupenda kwa banthu bonse kuchitike muli ziko lija. Ukukunali kupenda koyamba pamene Kilinas anali mukulu waboma mu silia.Koma aliyense anapita kumizinda yao ndi kukalembesa mazina yao.