Mon Dec 24 2018 16:03:57 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-12-24 16:03:57 +02:00
parent db7582e642
commit f2a96ebed3
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 20 \v 21 Pakuona chikulupilo chao, Yesu ananena, '' Mwamuna, machimo yako yakululukidwa.'' Akalembela ndiponso Afalisi banayamba kufunsa izi, ndikunena, ''Kodi ni ndani uyu wamene akamba manyozo
\v 20 \v 21 Pakuona chikulupilo chao, Yesu ananena, '' Mwamuna, machimo yako yakululukidwa.'' Akalembela ndiponso Afalisi banayamba kufunsa izi, ndikunena, ''Kodi ni ndani uyu wamene akamba manyozo? Ni ndani angakululukile machimo koma Mulungu eka?''