Mon Jan 14 2019 21:11:51 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-14 21:11:51 +02:00
parent 87f8ab6c2d
commit 9000bf17be
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 11 \v 12 \v 13 \v 14 \v 15 Kuchekela pamene apo Yesu anaenda kumuzinda wina oitanidwa Nani, Ndiopunzilabake ndiponso nagulu ikulu inaenda ndi iye. Pamene anafika pafupi ndikomo yamuzinda, Koma, mwamuna enzeokufa ananyamulidwa kuenda kunja, mwana mwamunaeka wamene bamaibake banali naye ( wamene anali ofedwwa), ndiponso gulu ikulu kuchoka mumuzinda banali ndi iye. Pamemene ambuye anamuona, Analiotengedwa ndichifundo paliemve ndiponso ananena kwaiye, '' kosalila.'' Ndiponso anapita kugwila mapulanga mwamene bananyamulila tupi, ndiponso bamene bana nyamula banaimilila.Ananena kwaiye, mwamuna wachichepele, ninena kwaiwe, nyamuka.'' Mwamuna wakufa anauka
\v 11 \v 12 \v 13 \v 14 \v 15 Kuchekela pamene apo Yesu anaenda kumuzinda wina oitanidwa Nani, Ndiopunzilabake ndiponso nagulu ikulu inaenda ndi iye. Pamene anafika pafupi ndikomo yamuzinda, Koma, mwamuna enzeokufa ananyamulidwa kuenda kunja, mwana mwamunaeka wamene bamaibake banali naye ( wamene anali ofedwwa), ndiponso gulu ikulu kuchoka mumuzinda banali ndi iye. Pamemene ambuye anamuona, Analiotengedwa ndichifundo paliemve ndiponso ananena kwaiye, '' kosalila.'' Ndiponso anapita kugwila mapulanga mwamene bananyamulila tupi, ndiponso bamene bana nyamula banaimilila.Ananena kwaiye, mwamuna wachichepele, ninena kwaiwe, nyamuka.'' Mwamuna wakufa anankala nakuyamba kukamba, ndiponso Yesu anamupasila kuli bamai bake