Mon Dec 24 2018 16:49:57 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-12-24 16:49:58 +02:00
parent af111ceae7
commit 777b23442d
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 29 \v 30 \v 31 \v 32 Koma Levi anapasa pwando ikulu kuli Yesu munyumba yake. Kunali bamisonko bambiri kujakumalo ndiponso banthu benangu banali kufendela kufupi na tebulo nakuyamba kudya ndi iye. Koma bafalisi ndiponso bakalembela banali kudandaula kubophunzila bake, nakunena, ''Kuti kodi nichani chamene udyela ndi kumwa nabamisonko ndiponso ndi ena ochimwa?'' Yesu anabayankha, ''Kuti banthu bamene sibanadwale sibangafune obachilisa, koma chabe bamene bodwala ndiye bangafune. Sininabwele
\v 29 \v 30 \v 31 \v 32 Koma Levi anapasa pwando ikulu kuli Yesu munyumba yake. Kunali bamisonko bambiri kujakumalo ndiponso banthu benangu banali kufendela kufupi na tebulo nakuyamba kudya ndi iye. Koma bafalisi ndiponso bakalembela banali kudandaula kubophunzila bake, nakunena, ''Kuti kodi nichani chamene udyela ndi kumwa nabamisonko ndiponso ndi ena ochimwa?'' Yesu anabayankha, ''Kuti banthu bamene sibanadwale sibangafune obachilisa, koma chabe bamene bodwala ndiye bangafune. Sininabwele kuitana bathu bolungama kulapila, koma kuitana ochimwa kulapila.''