nya-x-nyanja_luk_text_reg/02/45.txt

1 line
305 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 45 \v 46 \v 47 Pamene sibana mupeze, anabwelela ku Yelusalemu ndi kuyamba kumu sakila kuja.China bwela chachitika kuti pochokakela masiku yatatu, Bana mupeza mutempele, Enze nkhezi pakati ka apunzisi, kumvelela kwaiwo ndi kufunsa mafunso.Bonse banamumvela anadabwa pa kumvesesa kwake ndi mayankho yake.