nya-x-nyanja_jud_text_reg/01/20.txt

1 line
250 B
Plaintext

\v 20 Koma inu bokondedwa, zimangeni nhoka muchi khulupirilo chanu cho yela ngako, ndipo mupempele mu Muzimu Oyela. \v 21 Zisungeni mweka mu chikondi cha Mulungu, ndipo yembekezelani chifundo cha Ambuye watu Yesu Kristu chamene chileta umoyo osasila.