nya-x-nyanja_jud_text_reg/01/01.txt

1 line
219 B
Plaintext

\c 1 \v 1 Yuda, kapolo ya Yesu Kristu, ndipo mubale wa Yakobo, kwa abo boitanidwa, ndi bokondedwa mwa Tate Mulungu wathu, ndi osungidwa mwa Yesu Kristu: \v 2 Ndipo chifundo, mutendere ndi chikondi viyonjezelwepo pa inu.