Fri Nov 09 2018 16:44:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 16:44:45 +02:00
parent f63fd2ffe5
commit a3e2e32b62
3 changed files with 4 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 12 Aba ndiye bamene bazibisa mumagulu ya ma pwando yachikunja. Ba ma kondyelela kopanda nsoni, bangozidwesa bene beka. Nimakumbi yalimbe manzi, otengewa chabe na mpepo. Ni mitengo zamu ntawi yo panda mvula zilibe vipaso - bokufa kabili, bong'ámbika na mizu. \v 13 Ndi mafuunde oyipa pa chimana, bopanga manyazi yabo. Ni nyenyezi zosokera, zimene mudima wakuda unusungikila masiku osasila.
\v 12 Aba ndiye bamene bazibisa mumagulu ya ma pwando yachikunja. Ba ma kondyelela kopanda nsoni, bangozidwesa bene beka. Nimakumbi yalimbe manzi, otengewa chabe na mpepo. Ni mitengo zamu ntawi yo panda mvula zilibe vipaso - bokufa kabili, bong'ámbika na mizu. \v 13 Ndi mafuunde oyipa pa chimana, bopanga manyazi yabo. Ni nyenyezi zosokera, zimene mudima wakuda unusungiwa masiku osasila.

View File

@ -1 +1 @@
\v 14 Ndipo Enocki, wa nambala seveni kuchoka pa Adam, anapa uneneri pali beve ati, "Onani! Ambuye abwera ndi banthu bambiri makaana na makaana nabo yela bake. \v 15 Abwera kupasa chiwerudzo pamunthu onse. Abwera kugojensa bonse bamene bachita nchito zoyipa zamene bachitila mukuyipa kwao, ndipo na mau onse ya ntota yamene aba ba machimo banakamba kwa iye. \v 16 Aba ni bung'ung'uza, ba madandaulo, bamene bakonka zifunilo zao za uchimo. Ndipo ni ba vingazi, bamene pakuti vintu vibayendele mushe bekabeka, ba mazitutumula wina ndi muzake.
\v 14 Enocki, wa nambala seveni kuchoka pa Adam, anapa uneneri pali beve ati, "Onani! Ambuye abwera ndi banthu bambiri makaana na makaana nabo yela bake. \v 15 Abwera kupasa chiwerudzo pamunthu onse. Abwera kugojensa bonse bamene bachita nchito zoyipa zamene bachitila mukuyipa kwao, ndipo na mau onse ya ntota yamene aba ba machimo banakamba kwa iye. \v 16 Aba ni bung'ung'uza, ba madandaulo, bamene bakonka zifunilo zao za uchimo. Ndipo ni ba vingazi, bamene pakuti vintu vibayendele mushe bekabeka, ba mazitutumula wina ndi muzake.

View File

@ -42,6 +42,7 @@
"01-03",
"01-05",
"01-07",
"01-09"
"01-09",
"01-12"
]
}