Thu Jan 24 2019 15:54:35 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 15:54:35 +02:00
parent 2e92e2b3d8
commit 8738134adf
3 changed files with 3 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 27 \v 29 Pakuti onse amene munabatizidwa kwa Kristu munavela Kristu. \v 28 Muno mulibe myuda, kapena Greeki, muno mulibe kapolo, kapena omasuka, muno mulibe mwamuna ndi mkazi, pakuti muli onse mwa Kristu Yesu. Koma ngati muli a Kristu, inu muli mbeu za Abrahamu, nyumba monga mwa lonjezano.
\v 27 Pakuti onse amene munabatizidwa kwa Kristu munavela Kristu. \v 28 Muno mulibe myuda, kapena Greeki, muno mulibe kapolo, kapena omasuka, muno mulibe mwamuna ndi mkazi, pakuti muli onse mwa Kristu Yesu. \v 29 Koma ngati muli a Kristu, inu muli mbeu za Abrahamu, nyumba monga mwa lonjezano.

View File

@ -1 +1 @@
\c 4 \v 1 \v 2 Ine ndikunena kuti wolowa nyumba, akali mwana, sasiyana ndi kapolo, angankhale ndimwine waonse malowo onse. Koma iye ali pansi pa woyanganila ndi matrasiti mpaka tsiku yoikika kale ndi atate wake.
\c 4 \v 1 Ine ndikunena kuti wolowa nyumba, akali mwana, sasiyana ndi kapolo, angankhale ndimwine waonse malowo onse. \v 2 Koma iye ali pansi pa woyanganila ndi matrasiti mpaka tsiku yoikika kale ndi atate wake.

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Kotero, pamene ife tikali ana, ife tinali akapolo ku miyambo ya dziko lapansi. Koma pokwanilida nthawi, Mulungu anatuma Mwana wake, wobadwa ndi mkazi, wobadwa pansi la lamulo. Iye anachita izi kuti aombole iwo amene anali pansi ya lamulo, kuti ife tikalandile kutenga ngati ana.
\v 3 Kotero, pamene ife tikali ana, ife tinali akapolo ku miyambo ya dziko lapansi. \v 4 Koma pokwanilida nthawi, Mulungu anatuma Mwana wake, wobadwa ndi mkazi, wobadwa pansi la lamulo. \v 5 Iye anachita izi kuti aombole iwo amene anali pansi ya lamulo, kuti ife tikalandile kutenga ngati ana.